Nthambi yoona za nyengo ndi kusintha kwa nyengo yati madera a mchigawo chakumwera komanso pakati pa dziko lino ayembekezere mvula ya mphamvu komanso ya mabingu kuyambira m’mawa uno kufikila Lachisanu ...